Makalasi opanda Mipanda - pulogalamu yathu ya maphunziro!
Zikomo kwambiri chifukwa chochita chidwi ndi mileme! Tili ndi maphunziro asanu ndi atatu omwe takonzera inu. Zili ndi mfundo zambiri ndiponso zolimbikitsa zimene mungachite kuti musangalale ndi kuphunzira za mileme; malo omwe zimakhala, khalidwe yawo, ndiponso zinthu zomwe zingaike miyoyo yawo pachiwopsezo.
Chiyambi ku Makalasi Opanda Mipanda!
Kumanani ndi Spike, kazembe wathu wa mileme ndi abwenzi ake apamtima! Spike akuwonetsani pulogalamu yathu yamaphunziro.

intro_to_lessons__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1111 kb |
File Type: |
Mayankho achiyambi ku Makalasi Opanda Mipanda!
Kodi munazindikira kusiyana konse?
Kodi munazindikira kusiyana konse?

answers_-_intro_to_lessons__chichewa_.pdf | |
File Size: | 457 kb |
File Type: |
Phunziro 1 - Mleme ndi chiyani?
Takulandirani ku Phunziro 1! Spike ndi anzake akutengeni ku ulendo waku dziko lodabwitsa la Mileme!

lesson_1_-_what_is_a_bat__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1804 kb |
File Type: |
Mayankho a Phunziro 1 - Kodi mileme ndi chiyani?
Tikukhulupirira kuti mwasangalala ndi Phunziro 1! Awa ndi mayankho ake, tikukhulupiriranso kuti munachita bwino!

answers_to_lesson_1_-_what_is_a_bat__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1463 kb |
File Type: |
Phunziro 2 - Kusiyanasiyana kwa mileme!
Takulandirani ku Phunziro 2! Spike ndi anzake akuphunzitsani za mitundu yosiyanasiyana ya mileme ndi mabanja a mileme!

lesson_2_-_incredible_bat_diversity__chichewa_.pdf | |
File Size: | 2439 kb |
File Type: |
Mayankho a Phunziro 2 - Kusiyanasiyana kwa mileme
Tikukhulupirira kuti mwasangalala ndi Phunziro 2! Nawa mayankho.

answers_to_lesson_2_-_incredible_bat_diversity__chichewa_.pdf | |
File Size: | 337 kb |
File Type: |
Phunziro 3 - Kumene kumakhala mileme
Takulandirani ku Phunziro 3! Mu phunziro ili muphunzira za malo osiyanasiyana omwe mileme imakhala.

lesson_3_-_where_bats_live__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1662 kb |
File Type: |
Mayankho a Phunziro 3 - Komwe mileme imakhala
Tikukhulupirira kuti mwasangalala ndi Phunziro 3! Nawa mayankho.

answers_to_lesson_3_-_where_bats_live__chichewa_.pdf | |
File Size: | 673 kb |
File Type: |
Phunziro 4 - Zomwe mileme imadya
Takulandirani ku Phunziro 4! Mu phunziro ili mupeza zomwe mileme imapanga nazo nkhuli ndi zimene imakonda kudya.

lesson_4_-_what_bats_eat__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1307 kb |
File Type: |
Mayankho a Phunziro 4 - Zomwe mileme imadya
Tikukhulupirira kuti mwasangalala ndi Phunziro 4! Nawa mayankho.

answers_to_lesson_4_-_what_bats_eat__chichewa_.pdf | |
File Size: | 385 kb |
File Type: |
Phunziro 5 - Ana a mileme
Takulandirani ku Phunziro 5! M'phunziro lino muphunzira za ana a mileme ndi mmene amayi awo alili odabwitsa.

lesson_5_-_bat_babies__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1594 kb |
File Type: |
Mayankho a Phunziro 5 - Ana a mileme
Tikukhulupirira kuti mwasangalala ndi Phunziro 5! Nawa mayankho.

answers_to_lesson_5_-_bat_babies__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1118 kb |
File Type: |
Phunziro 6 - Zowulutsira zabwino kwambiri
Takulandirani ku Phunziro 6! Tili ndi phunziro labwino kwambiri, tiphunzira chifukwa chake mileme ili yopambana komanso yodabwitsa. Tili ndi vidiyo yosonyeza mileme ikuuluka pang'onopang'ono kuti muone mmene imaulukira. Mmodzi mwa anthu athu odzipereka (Anne Youngman) akuoneka m'vidiyoyi akuwerengetsanso mileme imene ikubwera kuchokera mokhala mwawo. Anne ali ndi chipangizo chopezera mileme kutero mudzamva kwa nthaŵi yochepa milemeyi ikulondola malo ake ndi mawu ake vidiyoyi isanayambe kusuntha pang'onopang'ono. Choncho muwona mileme ikuuluka, komanso momwe akatswiri osamala mileme amagwilira ntchito zawo.

![]()
|
|
Phunziro 7 - Zowopseza mileme
Takulandilani ku Phunziro 7, mudziphunzira za mavuto ndi zoopsa zimene mileme imakumana nazo. Moyo umakhala wovuta kwa mileme, choncho iyenera kukhala ndi abwenzi ambiri monga inu!

lesson_7_-_threats_to_bats__chichewa_.pdf | |
File Size: | 2300 kb |
File Type: |
Phunziro 8 - Momwe tingathandizire mileme
Takulandirani ku phunziro lathu lomalizira m'nkhani zanthu. Tikukhulupirira kuti mwasangalala nazo ndipo mwaphunzira zambiri zokhudza mileme, mmene ilili yapambana komanso chifukwa chomwe imafunikira abwenzi ambiri. M'phunziro lino, mudzaphunzira za zinthu zazing'ono kapena zazikulu zimene mungachite kuti muthandize mileme.

lesson_8_-_what_you_can_do_to_help_bats__chichewa_.pdf | |
File Size: | 1194 kb |
File Type: |